Luka 24:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Pamenepo anamugwadira ndi kubwerera ku Yerusalemu ali ndi chimwemwe chochuluka.+ 1 Petulo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngakhale kuti simunamuonepo, mumamukonda.+ Ngakhale simukumuona panopa, mumakhulupirira mwa iye ndipo mukusangalala kwambiri ndi chimwemwe chachikulu ndiponso chosaneneka,
8 Ngakhale kuti simunamuonepo, mumamukonda.+ Ngakhale simukumuona panopa, mumakhulupirira mwa iye ndipo mukusangalala kwambiri ndi chimwemwe chachikulu ndiponso chosaneneka,