Yohane 14:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mwandimva ndikukuuzani kuti, Ndikupita ndipo ndidzabweranso kwa inu. Ngati munali kundikonda, mukanakondwera kuti ndikupita kwa Atate wanga, chifukwa Atate ndi wamkulu+ kuposa ine. Yohane 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho inunso muli ndi chisoni panopa. Koma ndidzakuonaninso, ndipo mitima yanu idzasangalala.+ Palibenso amene adzathetse chimwemwe chanu. Machitidwe 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mmene iwo anali kuyang’anitsitsa kuthambo pamene iye anali kukwera kumwamba,+ panaonekera amuna awiri ovala zoyera+ ataimirira pambali pawo. Machitidwe 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo anabwerera+ ku Yerusalemu, kuchokera kuphiri lotchedwa phiri la Maolivi. Phiri limeneli lili pafupi ndi Yerusalemu, pa mtunda wa ulendo wa tsiku la sabata.*+
28 Mwandimva ndikukuuzani kuti, Ndikupita ndipo ndidzabweranso kwa inu. Ngati munali kundikonda, mukanakondwera kuti ndikupita kwa Atate wanga, chifukwa Atate ndi wamkulu+ kuposa ine.
22 Choncho inunso muli ndi chisoni panopa. Koma ndidzakuonaninso, ndipo mitima yanu idzasangalala.+ Palibenso amene adzathetse chimwemwe chanu.
10 Mmene iwo anali kuyang’anitsitsa kuthambo pamene iye anali kukwera kumwamba,+ panaonekera amuna awiri ovala zoyera+ ataimirira pambali pawo.
12 Pamenepo anabwerera+ ku Yerusalemu, kuchokera kuphiri lotchedwa phiri la Maolivi. Phiri limeneli lili pafupi ndi Yerusalemu, pa mtunda wa ulendo wa tsiku la sabata.*+