Machitidwe 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamene iwo ankayangʼanitsitsa kumwamba, iye akukwera kumwambako, mwadzidzidzi azibambo awiri ovala zoyera+ anaima pambali pawo. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:10 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, tsa. 11
10 Pamene iwo ankayangʼanitsitsa kumwamba, iye akukwera kumwambako, mwadzidzidzi azibambo awiri ovala zoyera+ anaima pambali pawo.