Mateyu 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Maonekedwe ake anali ngati a mphezi,+ ndipo zovala zake zinali zoyera mbee!+ Luka 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Atathedwa nzeru ndi zimenezi, anangoona amuna awiri ovala zovala zonyezimira ataima pambali pawo.+