Oweruza 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako mkaziyo anapita kukauza mwamuna wake kuti: “Munthu wa Mulungu woona anabwera kwa ine, ndipo maonekedwe ake anali ofanana ndi mngelo wa Mulungu woona,+ maonekedwe ochititsa mantha kwambiri.+ Koma sindinam’funse kumene wachokera ndiponso sanandiuze dzina lake.+ Danieli 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Thupi lake linali ngati mwala wa kulusolito,+ nkhope yake inali yowala ngati mphezi,+ maso ake anali kuoneka ngati miyuni yamoto,+ manja ake ndi mapazi ake zinali kuoneka ngati mkuwa wonyezimira,+ ndipo mawu ake anali kumveka ngati khamu la anthu.
6 Kenako mkaziyo anapita kukauza mwamuna wake kuti: “Munthu wa Mulungu woona anabwera kwa ine, ndipo maonekedwe ake anali ofanana ndi mngelo wa Mulungu woona,+ maonekedwe ochititsa mantha kwambiri.+ Koma sindinam’funse kumene wachokera ndiponso sanandiuze dzina lake.+
6 Thupi lake linali ngati mwala wa kulusolito,+ nkhope yake inali yowala ngati mphezi,+ maso ake anali kuoneka ngati miyuni yamoto,+ manja ake ndi mapazi ake zinali kuoneka ngati mkuwa wonyezimira,+ ndipo mawu ake anali kumveka ngati khamu la anthu.