Ezekieli 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Zamoyozo zinali kuyenda uku ndi uku, ndipo zikamayenda zinali kuoneka ngati mphezi.+ Mateyu 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumeneko iye anasandulika pamaso pawo, ndipo nkhope yake inawala ngati dzuwa.+ Malaya ake akunja anawala kwambiri.+
2 Kumeneko iye anasandulika pamaso pawo, ndipo nkhope yake inawala ngati dzuwa.+ Malaya ake akunja anawala kwambiri.+