2 Petulo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti iye analandira ulemu ndi ulemerero kuchokera kwa Mulungu Atate,+ pamene mawu anamveka kwa iye kuchokera mu ulemerero waukulu, kuti: “Uyu ndiye mwana wanga wokondedwa, amene ndikukondwera naye.”+ Chivumbulutso 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 M’dzanja lake lamanja anali ndi nyenyezi 7.+ M’kamwa mwake munali kutuluka lupanga lalitali, lakuthwa konsekonse.+ Nkhope yake inali yowala ngati dzuwa limene likuwala kwambiri.+
17 Pakuti iye analandira ulemu ndi ulemerero kuchokera kwa Mulungu Atate,+ pamene mawu anamveka kwa iye kuchokera mu ulemerero waukulu, kuti: “Uyu ndiye mwana wanga wokondedwa, amene ndikukondwera naye.”+
16 M’dzanja lake lamanja anali ndi nyenyezi 7.+ M’kamwa mwake munali kutuluka lupanga lalitali, lakuthwa konsekonse.+ Nkhope yake inali yowala ngati dzuwa limene likuwala kwambiri.+