Salimo 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iye anafika atakwera pakerubi wouluka.+Mulungu anali kuuluka mwaliwiro pamapiko a cholengedwa chauzimu.*+ Mateyu 24:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti mmene mphezi+ imang’animira kuchokera kum’mawa, ndi kuwala mpaka kumadzulo, zidzakhalanso choncho ndi kukhalapo kwa Mwana wa munthu.+
10 Iye anafika atakwera pakerubi wouluka.+Mulungu anali kuuluka mwaliwiro pamapiko a cholengedwa chauzimu.*+
27 Pakuti mmene mphezi+ imang’animira kuchokera kum’mawa, ndi kuwala mpaka kumadzulo, zidzakhalanso choncho ndi kukhalapo kwa Mwana wa munthu.+