24 Pakuti monga mphezi,+ mwa kung’anima kwake, imawala kuchokera mbali ina pansi pa thambo kukafika mbali ina pansi pa thambo, zidzakhalanso choncho ndi Mwana wa munthu.+
15 Pakuti tikukuuzani izi mogwirizana ndi mawu a Yehova+ kuti, ife amoyofe amene tidzakhalapo pa nthawi ya kukhalapo* kwa Ambuye,+ sitidzakhala patsogolo pa amene agona mu imfa.