Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Ndiyeno ndinapitiriza kuyang’ana kufikira pamene mipando yachifumu inaikidwa+ ndipo Wamasiku Ambiri+ anakhala pa mpando wake wachifumu. Zovala zake zinali zoyera kwambiri.+ Tsitsi lake linali looneka ngati ubweya wa nkhosa woyera.+ Mpando wake wachifumu unali kuyaka moto walawilawi,+ ndipo mawilo a mpandowo anali kuyaka moto.+

  • Habakuku 1:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Inu Yehova, inutu mwakhalapo kuyambira kalekale.+ Inu Mulungu wanga, Mulungu wanga Woyera, inu simufa.+ Inu Yehova, mwaika Akasidi pamalo oti muwaweruze. Inu Thanthwe,+ mwasankha kuti mutidzudzule.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena