Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 90:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Mapiri asanabadwe,+

      Kapena musanakhazikitse dziko lapansi+ ndi malo okhalapo anthu,*+

      Inu ndinu Mulungu kuyambira kalekale mpaka kalekale.+

  • Danieli 7:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Ndiyeno m’masomphenya ausikuwo, ndinaonanso wina wooneka ngati mwana wa munthu+ akubwera m’mitambo.+ Iye analoledwa kufika kwa Wamasiku Ambiri uja,+ ndipo anamubweretsa pafupi kwambiri ndi Iye.+

  • Danieli 7:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 kufikira Wamasiku Ambiri+ anabwera ndipo anapereka chiweruzo chokomera oyera a Wamkulukulu.+ Tsopano nthawi yoti oyerawo atenge ufumuwo inakwana, ndipo anautengadi.+

  • Habakuku 1:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Inu Yehova, inutu mwakhalapo kuyambira kalekale.+ Inu Mulungu wanga, Mulungu wanga Woyera, inu simufa.+ Inu Yehova, mwaika Akasidi pamalo oti muwaweruze. Inu Thanthwe,+ mwasankha kuti mutidzudzule.+

  • Chivumbulutso 4:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Zitatero, nthawi yomweyo ndinakhala mumphamvu ya mzimu, ndipo mpando wachifumu+ unaoneka uli pamalo ake kumwamba,+ wina atakhalapo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena