Salimo 90:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mapiri asanabadwe,+Kapena musanakhazikitse dziko lapansi+ ndi malo okhalapo anthu,*+Inu ndinu Mulungu kuyambira kalekale mpaka kalekale.+ Salimo 93:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mpando wanu wachifumu unakhazikika kalekale.+Munakhalako kuyambira kalekale.+ Chivumbulutso 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Ine ndine Alefa ndi Omega,”*+ akutero Yehova Mulungu, “Iye amene alipo, amene analipo, ndi amene akubwera,+ Wamphamvuyonse.”+
2 Mapiri asanabadwe,+Kapena musanakhazikitse dziko lapansi+ ndi malo okhalapo anthu,*+Inu ndinu Mulungu kuyambira kalekale mpaka kalekale.+
8 “Ine ndine Alefa ndi Omega,”*+ akutero Yehova Mulungu, “Iye amene alipo, amene analipo, ndi amene akubwera,+ Wamphamvuyonse.”+