Chivumbulutso 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso, mutu ndi tsitsi lake zinali zoyera+ ngati ubweya wa nkhosa woyera, zoyera kwambiri kuti mbee! Ndipo maso ake anali ngati lawi la moto.+
14 Komanso, mutu ndi tsitsi lake zinali zoyera+ ngati ubweya wa nkhosa woyera, zoyera kwambiri kuti mbee! Ndipo maso ake anali ngati lawi la moto.+