Salimo 104:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mwadzifunditsa kuwala ngati chofunda,+Mwatambasula kumwamba ngati nsalu ya chihema.+ Chivumbulutso 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye waloledwa kuvala zovala zapamwamba, zonyezimira ndi zoyera bwino, pakuti zovala zapamwambazo zikuimira ntchito zolungama za oyera.”+
2 Mwadzifunditsa kuwala ngati chofunda,+Mwatambasula kumwamba ngati nsalu ya chihema.+ Chivumbulutso 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye waloledwa kuvala zovala zapamwamba, zonyezimira ndi zoyera bwino, pakuti zovala zapamwambazo zikuimira ntchito zolungama za oyera.”+
8 Iye waloledwa kuvala zovala zapamwamba, zonyezimira ndi zoyera bwino, pakuti zovala zapamwambazo zikuimira ntchito zolungama za oyera.”+