Salimo 104:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mwadzifunditsa kuwala+ ngati chofunda,Mwatambasula kumwamba ngati nsalu yopangira tenti.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 104:2 Nsanja ya Olonda,8/15/2008, tsa. 13