Mateyu 24:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chifukwa mofanana ndi mmene mphezi imangʼanimira kuchokera kumʼmawa nʼkuwala mpaka kukafika kumadzulo, zidzakhalanso choncho ndi kukhalapo* kwa Mwana wa munthu.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:27 Nsanja ya Olonda,5/1/1993, tsa. 12
27 Chifukwa mofanana ndi mmene mphezi imangʼanimira kuchokera kumʼmawa nʼkuwala mpaka kukafika kumadzulo, zidzakhalanso choncho ndi kukhalapo* kwa Mwana wa munthu.+