Luka 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chifukwa mofanana ndi mphezi imene imangʼanima kuchokera mbali ina ya thambo kukafika mbali ina ya thambo, zidzakhalanso choncho ndi Mwana wa munthu+ mʼtsiku lake.+
24 Chifukwa mofanana ndi mphezi imene imangʼanima kuchokera mbali ina ya thambo kukafika mbali ina ya thambo, zidzakhalanso choncho ndi Mwana wa munthu+ mʼtsiku lake.+