Mateyu 24:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chifukwa mofanana ndi mmene mphezi imangʼanimira kuchokera kumʼmawa nʼkuwala mpaka kukafika kumadzulo, zidzakhalanso choncho ndi kukhalapo* kwa Mwana wa munthu.+
27 Chifukwa mofanana ndi mmene mphezi imangʼanimira kuchokera kumʼmawa nʼkuwala mpaka kukafika kumadzulo, zidzakhalanso choncho ndi kukhalapo* kwa Mwana wa munthu.+