Ekisodo 28:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mzere wa chinayi ukhale ndi miyala ya kulusolito,+ onekisi+ ndi yade. Zoikamo miyala zake zikhale zagolide.+ Ezekieli 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Maonekedwe a mawilowo+ anali ngati kuwala kwa mwala wa kulusolito,+ ndipo mawilo anayiwo anali ofanana. Kapangidwe kake kanali ngati kuti wilo lina lili pakati pa wilo linzake.*+ Chivumbulutso 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 achisanu wa sadonu, a 6 wa sadiyo, a 7 wa kulusolito,+ a 8 wa belulo, a 9 wa topazi,+ a 10 wa kulusopurazo, a 11 wa huwakinto, ndipo a 12, wa ametusito.*+
20 Mzere wa chinayi ukhale ndi miyala ya kulusolito,+ onekisi+ ndi yade. Zoikamo miyala zake zikhale zagolide.+
16 Maonekedwe a mawilowo+ anali ngati kuwala kwa mwala wa kulusolito,+ ndipo mawilo anayiwo anali ofanana. Kapangidwe kake kanali ngati kuti wilo lina lili pakati pa wilo linzake.*+
20 achisanu wa sadonu, a 6 wa sadiyo, a 7 wa kulusolito,+ a 8 wa belulo, a 9 wa topazi,+ a 10 wa kulusopurazo, a 11 wa huwakinto, ndipo a 12, wa ametusito.*+