-
Nyimbo ya Solomo 5:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Zala zake zonenepa bwino ndi zagolide, ndipo zikhadabo zake ndi zakulusolito. Mimba yake ndi yopangidwa ndi minyanga ya njovu yokutidwa ndi miyala ya safiro.
-