Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 28:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Uikepo miyala ndipo ikhale m’mizere inayi.+ Mzere woyamba ukhale ndi miyala ya rube,+ topazi+ ndi emarodi.+

  • Ekisodo 39:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno pachovala pachifuwacho anaikapo mizere inayi ya miyala. Mzere woyamba unali ndi miyala ya rube, topazi ndi emarodi.+

  • Yobu 28:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Sizingayerekezedwe ndi miyala ya topazi+ ya ku Kusi,

      Ngakhale golide woyenga bwino sangagulire nzeru.

  • Ezekieli 28:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Iwe unali mu Edeni, munda wa Mulungu.+ Unali kuvala chovala chokongoletsedwa ndi miyala yamtengo wapatali yamitundu yonse monga rube, topazi, yasipi, kulusolito, onekisi,+ yade, safiro, nofeki+ ndi emarodi. Zoikamo miyala imeneyi zinali zagolide. Anakukonzera zimenezi pa tsiku limene unalengedwa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena