Ekisodo 39:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno pachovala pachifuwacho anaikapo mizere inayi ya miyala. Mzere woyamba unali ndi miyala ya rube, topazi ndi emarodi.+ Chivumbulutso 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Maziko+ a mpanda wa mzindawo anawakongoletsa ndi miyala yamtengo wapatali ya mitundu yonse:+ maziko oyamba anali amwala wa yasipi,+ achiwiri wa safiro,+ achitatu wa kalikedo, achinayi wa emarodi,+
10 Ndiyeno pachovala pachifuwacho anaikapo mizere inayi ya miyala. Mzere woyamba unali ndi miyala ya rube, topazi ndi emarodi.+
19 Maziko+ a mpanda wa mzindawo anawakongoletsa ndi miyala yamtengo wapatali ya mitundu yonse:+ maziko oyamba anali amwala wa yasipi,+ achiwiri wa safiro,+ achitatu wa kalikedo, achinayi wa emarodi,+