Ekisodo 28:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Uikepo miyala ndipo ikhale m’mizere inayi.+ Mzere woyamba ukhale ndi miyala ya rube,+ topazi+ ndi emarodi.+
17 Uikepo miyala ndipo ikhale m’mizere inayi.+ Mzere woyamba ukhale ndi miyala ya rube,+ topazi+ ndi emarodi.+