Ekisodo 39:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno pachovala pachifuwacho anaikapo mizere inayi ya miyala. Mzere woyamba unali ndi miyala ya rube, topazi ndi emarodi.+
10 Ndiyeno pachovala pachifuwacho anaikapo mizere inayi ya miyala. Mzere woyamba unali ndi miyala ya rube, topazi ndi emarodi.+