Ezekieli 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndinapitiriza kuona masomphenya, ndipo ndinaona kuti pambali pa akerubi panali mawilo anayi. Pambali pa kerubi aliyense panali wilo limodzi.+ Maonekedwe a mawilowo anali ngati kuwala kwa mwala wa kulusolito.
9 Ndinapitiriza kuona masomphenya, ndipo ndinaona kuti pambali pa akerubi panali mawilo anayi. Pambali pa kerubi aliyense panali wilo limodzi.+ Maonekedwe a mawilowo anali ngati kuwala kwa mwala wa kulusolito.