Ekisodo 39:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo mzere wa chinayi+ unali ndi miyala ya kulusolito, onekisi+ ndi yade. Anaiika m’zoikamo zake zagolide. Danieli 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Thupi lake linali ngati mwala wa kulusolito,+ nkhope yake inali yowala ngati mphezi,+ maso ake anali kuoneka ngati miyuni yamoto,+ manja ake ndi mapazi ake zinali kuoneka ngati mkuwa wonyezimira,+ ndipo mawu ake anali kumveka ngati khamu la anthu.
13 Ndipo mzere wa chinayi+ unali ndi miyala ya kulusolito, onekisi+ ndi yade. Anaiika m’zoikamo zake zagolide.
6 Thupi lake linali ngati mwala wa kulusolito,+ nkhope yake inali yowala ngati mphezi,+ maso ake anali kuoneka ngati miyuni yamoto,+ manja ake ndi mapazi ake zinali kuoneka ngati mkuwa wonyezimira,+ ndipo mawu ake anali kumveka ngati khamu la anthu.