Chivumbulutso 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso, mutu ndi tsitsi lake zinali zoyera+ ngati ubweya wa nkhosa woyera, zoyera kwambiri kuti mbee! Ndipo maso ake anali ngati lawi la moto.+ Chivumbulutso 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Kwa mngelo wa mpingo wa ku Tiyatira+ lemba kuti: Izi ndi zimene Mwana+ wa Mulungu akunena, iye amene maso ake ali ngati lawi la moto,+ ndipo mapazi ake ali ngati mkuwa woyengedwa bwino.+
14 Komanso, mutu ndi tsitsi lake zinali zoyera+ ngati ubweya wa nkhosa woyera, zoyera kwambiri kuti mbee! Ndipo maso ake anali ngati lawi la moto.+
18 “Kwa mngelo wa mpingo wa ku Tiyatira+ lemba kuti: Izi ndi zimene Mwana+ wa Mulungu akunena, iye amene maso ake ali ngati lawi la moto,+ ndipo mapazi ake ali ngati mkuwa woyengedwa bwino.+