Chivumbulutso 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kwa mngelo wa mpingo wa ku Tiyatira+ lemba kuti: Izi ndi zimene Mwana wa Mulungu akunena, iye amene maso ake ali ngati lawi la moto+ ndipo mapazi ake ali ngati kopa* woyengedwa bwino:+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:18 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 47-48 Nsanja ya Olonda,5/15/2003, ptsa. 15-16
18 Kwa mngelo wa mpingo wa ku Tiyatira+ lemba kuti: Izi ndi zimene Mwana wa Mulungu akunena, iye amene maso ake ali ngati lawi la moto+ ndipo mapazi ake ali ngati kopa* woyengedwa bwino:+