Chivumbulutso 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso, mutu ndi tsitsi lake zinali zoyera+ ngati ubweya wa nkhosa woyera, zoyera kwambiri kuti mbee! Ndipo maso ake anali ngati lawi la moto.+ Chivumbulutso 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Maso ake anali ngati lawi la moto+ ndipo pamutu pake panali zisoti zachifumu+ zambiri. Anali ndi dzina+ lolembedwa limene wina aliyense sanali kulidziwa, koma iye yekha.
14 Komanso, mutu ndi tsitsi lake zinali zoyera+ ngati ubweya wa nkhosa woyera, zoyera kwambiri kuti mbee! Ndipo maso ake anali ngati lawi la moto.+
12 Maso ake anali ngati lawi la moto+ ndipo pamutu pake panali zisoti zachifumu+ zambiri. Anali ndi dzina+ lolembedwa limene wina aliyense sanali kulidziwa, koma iye yekha.