Ezekieli 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mapazi awo anali owongoka, ndipo kupansi kwa mapazi awo kunali ngati kupansi kwa mapazi a mwana wa ng’ombe.+ Mapaziwo anali kuwala ngati mkuwa wopukutidwa bwino.+ Chivumbulutso 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mapazi ake anali ngati mkuwa woyengedwa+ bwino ukamanyezimira m’ng’anjo, ndipo mawu+ ake anali ngati mkokomo wa madzi ambiri.
7 Mapazi awo anali owongoka, ndipo kupansi kwa mapazi awo kunali ngati kupansi kwa mapazi a mwana wa ng’ombe.+ Mapaziwo anali kuwala ngati mkuwa wopukutidwa bwino.+
15 Mapazi ake anali ngati mkuwa woyengedwa+ bwino ukamanyezimira m’ng’anjo, ndipo mawu+ ake anali ngati mkokomo wa madzi ambiri.