Chivumbulutso 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwa mzimu,+ ndinapezeka kuti ndili+ m’tsiku la Ambuye,+ ndipo kumbuyo kwanga ndinamva mawu amphamvu+ ngati kulira kwa lipenga.
10 Mwa mzimu,+ ndinapezeka kuti ndili+ m’tsiku la Ambuye,+ ndipo kumbuyo kwanga ndinamva mawu amphamvu+ ngati kulira kwa lipenga.