Ezekieli 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mapazi a angelowo anali owongoka ndipo anali ooneka ngati mapazi a mwana wa ngʼombe. Mapaziwo ankawala ngati kopa wopukutidwa bwino.+
7 Mapazi a angelowo anali owongoka ndipo anali ooneka ngati mapazi a mwana wa ngʼombe. Mapaziwo ankawala ngati kopa wopukutidwa bwino.+