Ezekieli 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mapazi awo anali owongoka, ndipo kupansi kwa mapazi awo kunali ngati kupansi kwa mapazi a mwana wa ng’ombe.+ Mapaziwo anali kuwala ngati mkuwa wopukutidwa bwino.+
7 Mapazi awo anali owongoka, ndipo kupansi kwa mapazi awo kunali ngati kupansi kwa mapazi a mwana wa ng’ombe.+ Mapaziwo anali kuwala ngati mkuwa wopukutidwa bwino.+