Danieli 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Thupi lake linali ngati mwala wa kulusolito,+ nkhope yake inali yowala ngati mphezi,+ maso ake anali kuoneka ngati miyuni yamoto,+ manja ake ndi mapazi ake zinali kuoneka ngati mkuwa wonyezimira,+ ndipo mawu ake anali kumveka ngati khamu la anthu. Chivumbulutso 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mapazi ake anali ngati mkuwa woyengedwa+ bwino ukamanyezimira m’ng’anjo, ndipo mawu+ ake anali ngati mkokomo wa madzi ambiri.
6 Thupi lake linali ngati mwala wa kulusolito,+ nkhope yake inali yowala ngati mphezi,+ maso ake anali kuoneka ngati miyuni yamoto,+ manja ake ndi mapazi ake zinali kuoneka ngati mkuwa wonyezimira,+ ndipo mawu ake anali kumveka ngati khamu la anthu.
15 Mapazi ake anali ngati mkuwa woyengedwa+ bwino ukamanyezimira m’ng’anjo, ndipo mawu+ ake anali ngati mkokomo wa madzi ambiri.