Ekisodo 39:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo mzere wa chinayi+ unali ndi miyala ya kulusolito, onekisi+ ndi yade. Anaiika m’zoikamo zake zagolide.
13 Ndipo mzere wa chinayi+ unali ndi miyala ya kulusolito, onekisi+ ndi yade. Anaiika m’zoikamo zake zagolide.