-
1 Mbiri 29:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ine ndakonzekera nyumba ya Mulungu wanga ndi mphamvu zanga zonse.+ Ndakonzekera+ golide+ wopangira zinthu zagolide, siliva wopangira zinthu zasiliva, mkuwa wopangira zinthu zamkuwa, zitsulo+ zopangira zinthu zachitsulo, ndi matabwa+ opangira zinthu zamatabwa. Ndakonzekeranso miyala ya onekisi,+ miyala yomanga ndi simenti yolimba, miyala yokongoletsera, miyala yamitundumitundu yamtengo wapatali, ndi miyala yambirimbiri ya alabasitala.
-