-
1 Mbiri 29:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ine ndayesetsa mwakhama kukonzekera nyumba ya Mulungu wanga. Ndapereka golide wodzapangira zinthu zagolide, siliva wodzapangira zinthu zasiliva, kopa* wodzapangira zinthu zakopa, zitsulo zodzapangira zinthu zachitsulo+ ndi matabwa+ odzapangira zinthu zamatabwa. Ndaperekanso miyala ya onekisi, miyala yomanga ndi simenti, miyala yokongoletsera, miyala yamtengo wapatali yamitundu yonse ndiponso miyala yambiri ya alabasitala.
-