1 Mbiri 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye anasonkhanitsanso matabwa osawerengeka a mkungudza,+ popeza Asidoni+ ndi anthu a ku Turo+ anali atabweretsera Davide matabwa ambirimbiri a mkungudza.
4 Iye anasonkhanitsanso matabwa osawerengeka a mkungudza,+ popeza Asidoni+ ndi anthu a ku Turo+ anali atabweretsera Davide matabwa ambirimbiri a mkungudza.