2 Mbiri 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo Solomo anatumiza uthenga kwa Hiramu+ mfumu ya Turo, kuti: “Monga momwe munachitira ndi Davide+ bambo anga pomawatumizira mitengo ya mkungudza kuti amangire nyumba yawo yokhalamo . . .
3 Ndipo Solomo anatumiza uthenga kwa Hiramu+ mfumu ya Turo, kuti: “Monga momwe munachitira ndi Davide+ bambo anga pomawatumizira mitengo ya mkungudza kuti amangire nyumba yawo yokhalamo . . .