11 Ndiyeno Hiramu+ mfumu ya Turo anatumiza amithenga+ kwa Davide. Anatumizanso mitengo ya mkungudza,+ anthu a ntchito zamatabwa ndi a ntchito za miyala yomangira khoma,* ndipo anayamba kumanga nyumba ya Davide.+
14Ndiyeno Hiramu+ mfumu ya Turo+ anatumiza amithenga kwa Davide. Anatumizanso matabwa a mkungudza,+ anthu omanga makoma, ndi anthu a ntchito zamatabwa kuti akamangire Davide nyumba.+