1 Mbiri 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atatero, Davide analamula kuti asonkhanitse alendo+ okhala m’dziko la Isiraeli. Alendowo anawaika kukhala osema miyala,+ kuti azisema miyala yofanana mbali zonse,+ yomangira nyumba ya Mulungu woona.
2 Atatero, Davide analamula kuti asonkhanitse alendo+ okhala m’dziko la Isiraeli. Alendowo anawaika kukhala osema miyala,+ kuti azisema miyala yofanana mbali zonse,+ yomangira nyumba ya Mulungu woona.