1 Mafumu 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 ana awo amene anatsala m’dzikomo, amene ana a Isiraeli analephera kuwawononga,+ Solomo anali kuwagwiritsa ntchito yaukapolo. Anthuwa akupitiriza kugwira ntchito yotere kufikira lero.+ 2 Mbiri 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako Solomo anawerenga amuna onse amene anali alendo m’dziko la Isiraeli.+ Anachita zimenezi pambuyo pa ntchito yowerenga alendowo imene Davide bambo ake anachita.+ Ndipo panapezeka amuna okwanira 153,600.
21 ana awo amene anatsala m’dzikomo, amene ana a Isiraeli analephera kuwawononga,+ Solomo anali kuwagwiritsa ntchito yaukapolo. Anthuwa akupitiriza kugwira ntchito yotere kufikira lero.+
17 Kenako Solomo anawerenga amuna onse amene anali alendo m’dziko la Isiraeli.+ Anachita zimenezi pambuyo pa ntchito yowerenga alendowo imene Davide bambo ake anachita.+ Ndipo panapezeka amuna okwanira 153,600.