1 Mafumu 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu amene Mfumu Solomo inawalemba ntchito yokakamiza anachokera ku Isiraeli konse, ndipo anthu olembedwa ntchito yokakamizawo+ anakwana amuna 30,000. 1 Mafumu 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inkawatumiza ku Lebanoni m’magulu a anthu 10,000 pamwezi. Kwa mwezi umodzi anthuwo ankakhala ku Lebanoni, ndipo kwa miyezi iwiri ankakhala kwawo.+ Adoniramu+ ndiye anali woyang’anira anthu olembedwa ntchito yokakamizawo.+ 2 Mbiri 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 ana onse ochokera kwa iwowa amene anatsala m’dzikomo, amene ana a Isiraeli sanawawononge,+ Solomo anali kuwagwiritsa+ ntchito yaukapolo, kufikira lero.+
13 Anthu amene Mfumu Solomo inawalemba ntchito yokakamiza anachokera ku Isiraeli konse, ndipo anthu olembedwa ntchito yokakamizawo+ anakwana amuna 30,000.
14 Inkawatumiza ku Lebanoni m’magulu a anthu 10,000 pamwezi. Kwa mwezi umodzi anthuwo ankakhala ku Lebanoni, ndipo kwa miyezi iwiri ankakhala kwawo.+ Adoniramu+ ndiye anali woyang’anira anthu olembedwa ntchito yokakamizawo.+
8 ana onse ochokera kwa iwowa amene anatsala m’dzikomo, amene ana a Isiraeli sanawawononge,+ Solomo anali kuwagwiritsa+ ntchito yaukapolo, kufikira lero.+