Yoswa 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Aefuraimu analephera kupitikitsa Akanani+ amene anali kukhala ku Gezeri.+ Choncho Akananiwo akukhalabe pakati pa Aefuraimu mpaka lero,+ ndipo anayamba kuwagwiritsa ntchito yaukapolo.+ 2 Mbiri 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako Solomo anawerenga amuna onse amene anali alendo m’dziko la Isiraeli.+ Anachita zimenezi pambuyo pa ntchito yowerenga alendowo imene Davide bambo ake anachita.+ Ndipo panapezeka amuna okwanira 153,600.
10 Aefuraimu analephera kupitikitsa Akanani+ amene anali kukhala ku Gezeri.+ Choncho Akananiwo akukhalabe pakati pa Aefuraimu mpaka lero,+ ndipo anayamba kuwagwiritsa ntchito yaukapolo.+
17 Kenako Solomo anawerenga amuna onse amene anali alendo m’dziko la Isiraeli.+ Anachita zimenezi pambuyo pa ntchito yowerenga alendowo imene Davide bambo ake anachita.+ Ndipo panapezeka amuna okwanira 153,600.