Yoswa 15:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Ana a Yuda analephera kupitikitsa+ Ayebusi+ omwe anali kukhala ku Yerusalemu,+ moti Ayebusi akukhalabe limodzi ndi ana a Yuda ku Yerusalemu mpaka lero. Yoswa 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana a Manase analephera kulanda mizindayi,+ moti Akanani anakakamira kukhalabe m’derali.+ Salimo 106:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Iwowa sanawononge mitundu ina ya anthu,+Mmene Yehova anawauzira.+
63 Ana a Yuda analephera kupitikitsa+ Ayebusi+ omwe anali kukhala ku Yerusalemu,+ moti Ayebusi akukhalabe limodzi ndi ana a Yuda ku Yerusalemu mpaka lero.