Oweruza 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno ana a Yuda anapitiriza kumenyana ndi mzinda wa Yerusalemu+ n’kuulanda. Anapha anthu okhala mmenemo ndi lupanga, ndipo mzindawo anautentha ndi moto. 1 Mbiri 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pambuyo pake Davide ndi Aisiraeli onse anapita ku Yerusalemu,+ kapena kuti ku Yebusi,+ dziko limene kunali kukhala Ayebusi.+
8 Ndiyeno ana a Yuda anapitiriza kumenyana ndi mzinda wa Yerusalemu+ n’kuulanda. Anapha anthu okhala mmenemo ndi lupanga, ndipo mzindawo anautentha ndi moto.
4 Pambuyo pake Davide ndi Aisiraeli onse anapita ku Yerusalemu,+ kapena kuti ku Yebusi,+ dziko limene kunali kukhala Ayebusi.+