Genesis 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anaberekanso Ayebusi,+ Aamori,+ Agirigasi, Genesis 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Aamori, Akanani, Agirigasi ndi la Ayebusi.”+ Ekisodo 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndikunenetsa kuti, ndidzakuchotsani mu nsautso+ ya Aiguputo ndi kukulowetsani m’dziko la Akanani, Ahiti, Aamori,+ Aperizi, Ahivi, ndi Ayebusi,+ dziko loyenda mkaka ndi uchi.”’+
17 Ndikunenetsa kuti, ndidzakuchotsani mu nsautso+ ya Aiguputo ndi kukulowetsani m’dziko la Akanani, Ahiti, Aamori,+ Aperizi, Ahivi, ndi Ayebusi,+ dziko loyenda mkaka ndi uchi.”’+