Genesis 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Mulungu anauza Abulamu kuti: “Udziwe ndithu kuti mbewu yako idzakhala mlendo m’dziko la eni,+ ndipo idzatumikira eni dzikolo. Iwo adzasautsa mbewu yako kwa zaka 400.+ Levitiko 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo kuti musakhale akapolo a Aiguputo.+ Ndinathyola goli lanu ndi kukuchititsani kuyenda mowongoka.+ Nehemiya 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Choncho inu munaona+ nsautso ya makolo athu ku Iguputo ndipo munamvanso kulira kwawo pa Nyanja Yofiira.+ Machitidwe 7:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ine ndaona ndithu mmene anthu anga amene ali ku Iguputo akuwazunzira.+ Ndamva kubuula kwawo+ ndipo ndatsika kudzawalanditsa.+ Tsopano tamvera. Ndikufuna ndikutume ku Iguputo.’+
13 Kenako Mulungu anauza Abulamu kuti: “Udziwe ndithu kuti mbewu yako idzakhala mlendo m’dziko la eni,+ ndipo idzatumikira eni dzikolo. Iwo adzasautsa mbewu yako kwa zaka 400.+
13 Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo kuti musakhale akapolo a Aiguputo.+ Ndinathyola goli lanu ndi kukuchititsani kuyenda mowongoka.+
9 “Choncho inu munaona+ nsautso ya makolo athu ku Iguputo ndipo munamvanso kulira kwawo pa Nyanja Yofiira.+
34 Ine ndaona ndithu mmene anthu anga amene ali ku Iguputo akuwazunzira.+ Ndamva kubuula kwawo+ ndipo ndatsika kudzawalanditsa.+ Tsopano tamvera. Ndikufuna ndikutume ku Iguputo.’+