Numeri 33:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Mukapitikitse anthu onse a m’dzikolo, ndipo mukawononge zifaniziro zawo zonse zamiyala,+ ndi mafano awo onse achitsulo.+ Mukawonongenso malo awo onse opatulika olambirira.+ Deuteronomo 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova Mulungu wako adzawapereka ndithu kwa iwe ndipo udzawagonjetse.+ Udzawawononge ndithu+ ndipo usadzachite nawo pangano kapena kuwakomera mtima.+ Oweruza 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo inu musachite pangano ndi anthu okhala m’dziko ili,+ m’malomwake mugwetse maguwa awo ansembe.’+ Koma inu simunamvere mawu anga.+ N’chifukwa chiyani mwachita zimenezi?+
52 Mukapitikitse anthu onse a m’dzikolo, ndipo mukawononge zifaniziro zawo zonse zamiyala,+ ndi mafano awo onse achitsulo.+ Mukawonongenso malo awo onse opatulika olambirira.+
2 Yehova Mulungu wako adzawapereka ndithu kwa iwe ndipo udzawagonjetse.+ Udzawawononge ndithu+ ndipo usadzachite nawo pangano kapena kuwakomera mtima.+
2 Ndipo inu musachite pangano ndi anthu okhala m’dziko ili,+ m’malomwake mugwetse maguwa awo ansembe.’+ Koma inu simunamvere mawu anga.+ N’chifukwa chiyani mwachita zimenezi?+