Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 27:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Munthu aliyense woperekedwa kwa Mulungu kuti awonongedwe sangathe kuwomboledwa.+ Ameneyo aziphedwa ndithu.+

  • Deuteronomo 20:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 chifukwa muyenera kuwawononga ndithu. Mukawononge Ahiti, Aamori, Akanani, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi,+ monga mmene Yehova Mulungu wanu anakulamulirani.

  • Yoswa 6:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mzindawu wapatulidwa kuti uwonongedwe,+ pakuti mzindawu limodzi ndi zonse zili mmenemo ndi za Yehova. Rahabi+ yekha, hule uja, musamuphe. Mum’siye ndi moyo, iye pamodzi ndi onse amene ali naye m’nyumba mwake, chifukwa iye anabisa azondi amene tinawatuma.+

  • Yoswa 10:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Yoswa analanda mzinda wa Makeda+ tsiku limenelo ndipo anapha anthu a mumzindawo ndi lupanga. Mfumu ya mzindawo ndi anthu ake onse anawapha,+ ndipo Yoswa anaonetsetsa kuti pasakhale wopulumuka. Mfumu ya ku Makeda+ anaichita zofanana ndi zomwe anachita mfumu ya ku Yeriko.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena